Opikisana pa mpando wa utsogoleri wa dziko asanamizire kuti Mulungu waatuma – Chaima
M'modzi mwa olankhulapo pa nkhani za ndale ndi ulamuliro wabwino, George Chaima wati onse amene akudzapikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wa dziko, asamanamizile kuti atumidwa ndi Mulungu, ponena kuti ngati atumidwa ndi Mulungu akuyenera… ...
